Mawu a M'munsi
a Akhristu oona ayenera ‘kutsatira mapazi a [Yesu] mosamala kwambiri.’ Kodi iye anatisiyira “chitsanzo” chotani chimene tiyenera kutsatira? Munkhaniyi tipeza yankho la funso limeneli. Tikambirananso chifukwa chake tiyenera kutsatira mapazi ake mosamala kwambiri komanso mmene tingachitire zimenezi.