Mawu a M'munsi
a Kodi tingatani kuti tizionabe utumiki wathu moyenera ngakhale pamene anthu ambiri sapezeka pakhomo kapenanso sasangalala ndi uthenga wathu? Nkhaniyi itithandiza kudziwa zimene tingachite kuti tizisangalalabe pamene tikugwira ntchito yolalikira.