Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano

Mawu a M'munsi

c MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: (Kuchokera pamwamba mpaka pansi): M’bale ndi mkazi wake akulalikira m’dera limene ndi zovuta kupeza anthu panyumba. Khomo loyamba mwiniwake wapita ku ntchito, wa khomo lachiwiri wapita kuchipatala ndipo wa khomo lachitatu wapita kukagula zinthu. Kenako akwanitsa kulalikira kwa munthu wa khomo loyamba uja atapitako pa nthawi ina pa tsikulo. Munthu wa khomo lachiwiri uja akumana naye pamene akulalikira m’malo opezeka anthu ambiri pafupi ndi chipatala. Ndipo akulalikira munthu wa khomo lachitatu lija pomuimbira foni.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani