Mawu a M'munsi
a Yehova watipatsa mwayi, osati wogwira ntchito yolalikira yokha, koma kutinso tiziphunzitsa anthu kusunga zinthu zonse zimene Yesu analamula. Ndiye n’chiyani chimatilimbikitsa kuti tiziphunzitsa ena? Kodi ndi mavuto otani amene timakumana nawo tikamalikira komanso kuphunzitsa anthu kuti akhale otsatira a Yesu? Nanga tingatani kuti mavutowo asatilepheretse kugwira ntchitoyi? Munkhaniyi, tikambirana mayankho a mafunso amenewa.