Mawu a M'munsi
b Kuti mudziwe zambiri pa nkhani yokhudza zimene aliyense angachite pothandiza anthu kuti akhale ophunzira a Yesu, onani nkhani yakuti, “Aliyense Mumpingo Angathandize Ophunzira Baibulo Kuti Abatizidwe,” yomwe ili mu Nsanja ya Olonda ya March 2021.