Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano

Mawu a M'munsi

b MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Chifukwa choti analengedwa m’chifaniziro cha Mulungu, mwamuna ndi mkazi wake amakondana ndiponso amakonda ana awo. Banjali limakondanso Yehova. Iwo akusonyeza kuyamikira mwayi wokhala ndi ana pothandiza anawo kuti azikonda komanso kutumikira Yehova. Makolowa akugwiritsa ntchito vidiyo pofotokozera ana awo chifukwa chake Yehova anapereka Yesu monga dipo. Akuphunzitsanso anawo kuti m’Paradaiso akubwerayo, tizidzasamalira dzikoli komanso nyama mpaka kalekale.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani