Mawu a M'munsi
a Achikulire okhulupirika ali ngati chuma chamtengo wapatali. Nkhaniyi itilimbikitsa kuti tiziwayamikira kwambiri komanso tikambirana zimene tingachite kuti tizipindula kwambiri ndi nzeru zawo ndiponso zimene amadziwa. Ithandizanso achikulire kuona kuti gulu la Yehova limawaona kukhala ofunika kwambiri.