Mawu a M'munsi
a M’mipingo yathu muli achinyamata ambiri omwe akuyesetsa kuthandiza gulu la Yehova. Posatengera chikhalidwe chawo komanso kumene anakulira, achikulire angathandize achinyamatawa kugwiritsa ntchito mphamvu zawo zonse kutumikira Yehova.