Mawu a M'munsi a Nkhaniyi ikufotokoza kamvedwe katsopano ka lemba la Hagai 2:7. Tiphunzira zimene tingachite kuti tizigwira nawo ntchito yosangalatsa imene ikugwedeza mitundu yonse ya anthu. Tionanso kuti anthu ena amamvetsera uthenga wabwino chifukwa cha ntchito yogwedezayi pomwe ena amadana nayo.