Mawu a M'munsi
c Zimenezi zikusintha zimene tinkakhulupirira m’mbuyomu. Poyamba tinkanena kuti anthu oona mtima sayamba kutumikira Yehova chifukwa cha ntchito yogwedeza mitundu yonse ya anthu. Onani “Mafunso Ochokera kwa Owerenga” mu Nsanja ya Olonda ya May 15, 2006.