Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Hagai analimbikitsa anthu a Mulungu kuchita khama pa ntchito yomanganso kachisi ndipo masiku anonso anthu a Mulungu amachita khama kulengeza uthenga wabwino. Banja likugwira nawo ntchito imene ikugwedeza dziko lonse yonena za kugwedeza komaliza kumene kukubwera.