Mawu a M'munsi
a Chifundo ndi limodzi mwa makhalidwe abwino kwambiri a Yehova ndiponso ndi khalidwe limene tonsefe tiyenera kukhala nawo. Munkhaniyi tikambirana zimene zimachititsa Yehova kuti azisonyeza chifundo, chifukwa chake tinganene kuti chilango chimasonyeza chifundo chake komanso zimene tingachite kuti tizitsanzira khalidwe labwinoli.