Mawu a M'munsi
a Munkhaniyi tikambirana zokhudza kulambira koona kumene Yesu anakhazikitsa komanso zimene ophunzira ake ankachita potsatira kulambira koonako. Tionanso umboni wakuti masiku ano a Mboni za Yehova amatsatira kulambira koona kumeneko.