Mawu a M'munsi
a Tikuyembekezera mwachidwi kuti dziko loipali liwonongedwa posachedwapa. Koma mwina nthawi zina tingamakayikire ngati chikhulupiriro chathu chidzakhalebe cholimba pa nthawiyo. Munkhaniyi tikambirana zitsanzo za anthu ena komanso mfundo zomwe zingatithandize kuti tilimbitse chikhulupiriro chathu panopa.