Mawu a M'munsi
a Yehova amafuna tizisonyeza chikondi chokhulupirika kwa abale ndi alongo athu mumpingo. Tingamvetse bwino zimene munthu amene ali ndi chikondi chokhulupirika amachita, tikaganizira mmene atumiki ena a Mulungu m’mbuyomu ankasonyezera khalidweli. Munkhaniyi tiona zimene tingaphunzire pachitsanzo cha Rute, Naomi komanso Boazi.