Mawu a M'munsi
b Munkhaniyi komanso yapita ija, sitinakambirane mavesi omwe amanena za tsankho, miseche, kudya magazi, kukhulupirira mizimu, kulosera zam’tsogolo komanso khalidwe la chiwerewere.—Lev. 19:15, 16, 26-29, 31.—Onani nkhani yakuti “Mafunso Ochokera kwa Owerenga,” yomwe ili m’magaziniyi.