Mawu a M'munsi
b MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: M’bale ntchito yamuthera, alibe ndalama zothandizira banja lake komanso akufunika kupeza nyumba. Ngati sangasamale akhoza kumangokhalira kuda nkhawa n’kusiya kuika pamalo oyamba zinthu zokhudza kulambira.