Mawu a M'munsi
a Kaya tikuyembekezera kudzapita kumwamba kapena kudzakhala m’Paradaiso padzikoli, timayembekezera mwachidwi kuchita Chikumbutso chaka chilichonse. Munkhaniyi tikambirana zifukwa zomveka zochokera m’Malemba zotichititsa kupezeka pamwambowu komanso mmene timapindulira tikapezekapo.