Mawu a M'munsi
a Nkhaniyi itithandiza kuona chifukwa chake tiyenera kumakhulupirira kwambiri Yehova ndi anthu amene amatsogolera gulu lake padzikoli. Tionanso mmene kuchita zimenezi kungatithandizire panopa komanso kutikonzekeretsa pa mavuto omwe tidzakumane nawo m’tsogolo.