Mawu a M'munsi
a Anthu a Yehova amazindikira kufunika kotsatira malangizo a m’Baibulo. Komabe si nthawi zonse pamene zimakhala zophweka kuvomereza malangizo. N’chifukwa chiyani zili choncho? Ndipo n’chiyani chingatithandize kuti tizipindula ndi malangizo amene timalandira?