Mawu a M'munsi
a Si nthawi zonse pamene zimakhala zophweka kupereka malangizo. Ndiye kodi tingatani kuti tiziwapereka m’njira yoti akhale othandiza komanso olimbikitsa kwa ena? Nkhaniyi ithandiza makamaka akulu kuti azipereka malangizo kwa ena mowafika pamtima.