Mawu a M'munsi
a Nthawi zonse Yesu ankaika zofuna za ena patsogolo osati zake. Munkhaniyi tikambirana mmene tingamutsanzirire. Tikambirananso madalitso amene tingapeze chifukwa chotsanzira mtima wa Yesu wofunitsitsa kuthandiza ena.