Mawu a M'munsi b TANTHAUZO LA MAWU ENA: ‘Kuvula umunthu wakale,’ kumatanthauza kusiya makhalidwe ndi zizolowezi zimene sizisangalatsa Yehova ndipo tiyenera kuchita zimenezi tisanabatizidwe.—Aef. 4:22.