Mawu a M'munsi
a Buku la Chivumbulutso limagwiritsa ntchito zizindikiro potithandiza kudziwa adani a Mulungu. Buku la Danieli limatithandiza kumvetsa tanthauzo la zizindikirozi. Munkhaniyi tiyerekezera maulosi ena m’bukuli ofanana ndi omwe ali m’buku la Chivumbulutso. Izi zitithandiza kudziwa adani a Mulungu. Kenako tikambirana zomwe zidzawachitikire.