Mawu a M'munsi
c Mosiyana ndi chilombo choyamba chija, chifaniziro chake chilibe ‘zisoti zachifumu’ panyanga zake. (Chiv. 13:1) Zimenezi zili choncho chifukwa ‘chatuluka mwa mafumu 7 aja’ ndipo chimadalira mafumuwo kuti achipatse ulamuliro.—Onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Chilombo Chofiira Kwambiri Chomwe Chimatchulidwa M’chaputala 17 cha Chivumbulutso Chimaimira Chiyani?”