Mawu a M'munsi
a Solomo ndi Yesu anali anthu anzeru kwambiri. Yehova Mulungu ndi amene anawapatsa nzeruzi. Munkhaniyi tiona malangizo omwe Solomo ndi Yesu anapereka okhudza kudziona moyenera, komanso kuona moyenera ndalama ndi ntchito. Tionanso mmene Akhristu anzathu apindulira chifukwa chogwiritsa ntchito malangizo anzeru opezeka m’Baibulo amenewa.