Mawu a M'munsi
a Makolo a Chikhristu amakonda kwambiri ana awo. Amachita khama kuwapezera zinthu zofunika pa moyo komanso kuwathandiza kuti azisangalala. Chofunika kwambiri n’chakuti iwo amachita zonse zomwe angathe pothandiza anawo kuti azikonda kwambiri Yehova. Nkhaniyi ifotokoza mfundo 4 za m’Baibulo zomwe zingathandize makolo kuchita zimenezi.