Mawu a M'munsi
b TANTHAUZO LA MAWU ENA: Mawu a Chiheberi omwe anawamasulira kuti “chiyembekezo” kwenikweni amatanthauza “kudikira” chinachake mwachidwi. Angatanthauzenso kukhulupirira wina wake kapena kumudalira.—Sal. 25:2, 3; 62:5.