Mawu a M'munsi
a Yehova anasankhanso mngelo amene “ankayenda patsogolo pa Aisiraeli” powatsogolera ku Dziko Lolonjezedwa. N’zodziwikiratu kuti ameneyu ndi Mikayeli, lomwe ndi dzina limene Yesu amadziwika nalo kumwamba.—Eks. 14:19; 32:34.