Mawu a M'munsi
e M’zikhalidwe zina, m’bale ndi amene amafunsira mlongo kuti ayambe chibwenzi. Koma palibenso vuto ngati mlongo atafunsira m’bale. (Rute 3:1-13) Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani yakuti, “Achinyamata Akufunsa Kuti . . . Kodi Mnyamata Ndingamuuze Bwanji Kuti Ndikumufuna?” mu Galamukani! ya November 8, 2004.