Mawu a M'munsi
e Tikudziwa kuti nkhani ya kulambira ndi yofunika kwambiri kwa Yehova chifukwa chakuti malamulo awiri oyamba mu Chilamulo cha Mose ankaletsa kulambira munthu kapena chinthu chilichonse koma Yehova yekha.—Eks. 20:1-6.