Mawu a M'munsi b Ngati mwana wanu anamaliza kuphunzira buku la Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, mungabwereze naye mitu ina ya m’gawo 3 ndi 4 yomwe imafotokoza mfundo za m’Baibulo za makhalidwe abwino.