Mawu a M'munsi b Madzi amene Yesu anatchula amaimira zinthu zimene Yehova amatipatsa kuti tidzapeze moyo wosatha.