October Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 2017 Zitsanzo za Ulaliki October 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | DANIELI 7-9 Ulosi wa Danieli Unaneneratu Nthawi Imene Mesiya Adzafike MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Tingatani Kuti Tiziphunzira Malemba Mwakhama October 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | DANIELI 10-12 Yehova Ananeneratu Zokhudza Mafumu a Mtsogolo October 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | HOSEYA 1-7 Kodi Mumasangalala ndi Chikondi Chokhulupirika Ngati Mmene Yehova Amachitira? October 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | HOSEYA 8-14 Muzipereka Zinthu Zabwino Kwambiri kwa Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzitumikira Yehova Nthawi Zonse October 30–November 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOWELI 1-3 “Ana Anu Aamuna ndi Ana Anu Aakazi Adzanenera”