August Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya August 2018 Zimene Tinganene August 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 17-18 Muzisonyeza Kuyamikira MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kumbukirani Mkazi wa Loti August 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 19-20 Zomwe Tikuphunzira M’fanizo la Ndalama 10 za Mina MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Yesetsani Kudziwa Bwino Webusaiti Yathu ya JW.ORG August 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 21-22 “Chipulumutso Chanu Chikuyandikira” August 27–September 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 23-24 Muzikhala Okonzeka Kukhululuka MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yesu Anaferanso M’bale Wakoyo