February Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya February 2019 Zimene Tinganene February 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 1-3 Pitirizani Kuphunzitsa Chikumbumtima Chanu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mumaona Makhalidwe a Mulungu Osaoneka ndi Maso? February 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 4-6 “Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake Kwa Ife” February 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 7-8 Kodi ‘Mukudikira Mwachidwi’? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Pitirizani Kudikira Mopirira February 25–March 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 9-11 Fanizo la Mtengo wa Maolivi MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kusiya Kuphunzira ndi Munthu Yemwe Sakupita Patsogolo