January Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya January 2019 Zimene Tinganene January 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 21-22 “Chifuniro cha Yehova Chichitike” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Anatithandiza Kulera Ana Athu January 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 23-24 Anaimbidwa Mlandu Wosokoneza Anthu Komanso Kuukira Boma January 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 25-26 Paulo Anapempha Kukaonekera kwa Kaisara Ndipo Kenako Analalikira Mfumu Herode Agiripa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Lamulo Lovomereza Ntchito Yathu Yolalikira ku Quebec January 28–February 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 27-28 Paulo Anapita ku Roma MOYO WATHU WACHIKHRISTU ‘Paulo Anayamika Mulungu, Ndipo Analimba Mtima’