July Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, July-August 2021 July 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambira Bwanji? KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muzisonyeza Kuti Mumawaganizira July 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka? MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Musamade Nkhawa” July 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mfundo Zothandiza Kuweruza Milandu Mwachilungamo July 26–August 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amaona Kuti Moyo wa Munthu Ndi Wamtengo Wapatali August 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Zinyama? KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muziwafika Pamtima August 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Akazi? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Uziona Akazi Achikulire Ngati Amayi Ako, Akazi Achitsikana Ngati Alongo Ako August 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU ‘Madalitso Onsewa . . . Adzakupeza’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mmene Chilengedwe Chimasonyezera Kuti Mulungu Ndi Wachikondi August 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kutumikira Yehova Sikovuta Kwambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kukhala Olimba Mtima Sikovuta Kwambiri August 30–September 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Tingaphunzire pa Mafanizo a mu Nyimbo Youziridwa KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene