May Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, May-June 2021 May 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera May 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzikwaniritsa Zimene Mwalonjeza May 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU ‘Mukathamangitse Anthu Onse a M’dzikolo’ KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muzigwiritsa Ntchito Mafanizo May 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Thawirani kwa Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kupatsidwa Chilango Kumasonyeza Kuti Yehova Amatikonda May 31–June 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Mukuweruzira Mulungu” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Khalanibe Okonzeka Pamene Tili Kumapeto kwa “Masiku Otsiriza” June 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Malamulo a Yehova Amasonyeza Kuti Ndi Wanzeru Komanso Wachilungamo KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muziphunzitsa Ndi Mtima Wonse June 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzisonyeza Chikondi M’banja June 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Usadzachite Nawo Mgwirizano wa Ukwati” June 28–July 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzichita Chiyani?” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzisankha Zinthu Mwanzeru pa Nkhani ya Mowa KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene