November Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, November-December 2021 November 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Anachita Zinthu Mwanzeru Pogawa Malo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Timathokoza Yehova Chifukwa cha Chikondi Chanu November 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Tingaphunzire pa Kusamvana kwa Mafuko a Aisiraeli November 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mawu Omaliza Amene Yoswa Analimbikitsa Nawo Mtundu wa Aisiraeli November 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Yochititsa Chidwi KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muzilola Kuti Yehova Azikuthandizani Kudzera M’pemphero MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mfundo Zothandiza Kuti Msonkhano Wokonzekera Utumiki Uzikhala Wabwino November 29–December 5, 2021 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Alongo Angatani Kuti Azichita Zambiri Potumikira Yehova? December 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Ntchito Yovuta Yomwe Inatheka Ndi Mzimu Woyera December 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada December 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yefita Anali Munthu Wauzimu December 27, 2021–January 2, 2022 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Makolo Angaphunzire Chiyani kwa Manowa ndi Mkazi Wake? KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI Muzithandiza Ophunzira Anu Kuti Azidzidyetsa Mwauzimu KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene