November Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, November-December 2022 November 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo” MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Khalani Opatsa” November 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Anachita Zimene Anthu Sankayembekezera November 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zimene Zingatithandize Kuti Tisamazengereze Pochita Zinthu November 28–December 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa CHUMA CHOPEZEKA MMAWU A MULUNGU “Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe”—2Mf 9:8 MOYO WATHU WACHIKHRISTU N’chifukwa Chiyani Akhristu Akufunika Kuyesetsa Kuti Akhale Ndi Zolinga? December 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kuchita Zinthu Ndi Mtima Wonse Kumabweretsa Madalitso Ambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Sangaiwale Khama Limene Tinachita Pomutumikira December 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muziyembekezera Mapeto a Dzikoli Molimba Mtima December 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Adani Athu Amachita Pofuna Kutifooketsa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzisangalala Mukamazunzidwa December 26–January 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Pemphero Linachititsa Yehova Kuchitapo Kanthu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mapemphero Athu ndi Amtengo Wapatali kwa Yehova KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene