YOSWA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Yoswa anatumiza anthu awiri kukafufuza zokhudza Yeriko (1-3)
Rahabi anabisa anthu okafufuza (4-7)
Analonjeza Rahabi (8-21a)
Okafufuza zokhudza mzinda anabwerera kwa Yoswa (21b-24)
3
4
5
Mdulidwe ku Giligala (1-9)
Chikondwerero cha Pasika; mana anasiya (10-12)
Kalonga wa gulu lankhondo la Yehova (13-15)
6
7
Aisiraeli anagonjetsedwa ku Ai (1-5)
Pemphero la Yoswa (6-9)
Aisiraeli anagonjetsedwa chifukwa cha tchimo (10-15)
Tchimo la Akani linadziwika, anaponyedwa miyala (16-26)
8
Yoswa anatumiza anthu oti akabisalire anthu a ku Ai (1-13)
Mzinda wa Ai unagonjetsedwa (14-29)
Chilamulo chinawerengedwa paphiri la Ebala (30-35)
9
Agibiyoni ochenjera anapempha mgwirizano (1-15)
Bodza la Agibiyoni linadziwika (16-21)
Agibiyoni anakhala otola nkhuni ndi kutunga madzi (22-27)
10
Aisiraeli anathandiza Agibiyoni (1-7)
Yehova anamenyera nkhondo Aisiraeli (8-15)
Mafumu 5 anaphedwa (16-28)
Analanda mizinda yakumʼmwera (29-43)
11
12
13
Madera amene anali asanalandidwe (1-7)
Kugawa malo a kumʼmawa kwa Yorodano (8-14)
Cholowa cha fuko la Rubeni (15-23)
Cholowa cha fuko la Gadi (24-28)
Cholowa cha Manase, kumʼmawa kwa Yorodano (29-32)
Yehova ndi cholowa cha Alevi (33)
14
15
Cholowa cha fuko la Yuda (1-12)
Mwana wamkazi wa Kalebe analandira malo (13-19)
Mizinda ya anthu a fuko la Yuda (20-63)
16
17
18
19
Cholowa cha fuko la Simiyoni (1-9)
Cholowa cha fuko la Zebuloni (10-16)
Cholowa cha fuko la Isakala (17-23)
Cholowa cha fuko la Aseri (24-31)
Cholowa cha fuko la Nafitali (32-39)
Cholowa cha fuko la Dani (40-48)
Cholowa cha Yoswa (49-51)
20
21
22
Mafuko akumʼmawa anabwerera kwawo (1-8)
Anamanga guwa ku Yorodano (9-12)
Anafotokoza cholinga cha guwa (13-29)
Anagwirizananso (30-34)
23
24
Yoswa anafotokoza mbiri ya Aisiraeli (1-13)
Anawalimbikitsa kutumikira Yehova (14-24)
Yoswa anachita pangano ndi Aisiraeli (25-28)
Yoswa anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda (29-31)
Mafupa a Yosefe anaikidwa mʼmanda ku Sekemu (32)
Eliezara anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda (33)