Mose ndi Aroni akuchita zozizwitsa pamaso pa Farao
Zimene Tinganene
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi timadziwa bwanji kuti mavuto omwe timakumana nawo si chilango chochokera kwa Mulungu?
Lemba: Yak 1:13
Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani timavutika?
○● ULENDO WOBWEREZA
Funso: N’chifukwa chiyani timavutika?
Lemba: 1Yo 5:19
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amamva bwanji akamationa tikuvutika?