LAYIBULARE YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAYIBULARE YA PA INTANETI
Chitumbuka
  • BAIBOLO
  • MABUKU
  • MAUNGANO
  • w00 12/1 p. 30
  • Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000

Vidiyo palije.

Phepani, pali suzgo linyake.

  • Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000
  • Gongwe la Mulinda Likupharazga Ufumu wa Yehova—2000
  • Mitu Yichoko
  • BAIBULO
  • MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
  • MBONI ZA YEHOVA
  • MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
  • MBIRI YA MOYO WANGA
  • NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
  • NKHANI ZOSIYANASIYANA
  • OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
  • YEHOVA
  • YESU KRISTU
Gongwe la Mulinda Likupharazga Ufumu wa Yehova—2000
w00 12/1 p. 30

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000

Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo

BAIBULO

Buku Labwino? 12/1

Chaka Chabwino Kwambiri Kugaŵira, 1/15

Mauthenga Abwino—Mbiri Kapena Nthano? 5/15

Mauthenga Obisika? 4/1

MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA

Anadandaula Ndani za Mafuta Amene Yesu Anadzozedwa? 4/15

Angakane Kusudzulidwa, 12/15

Kodi Kunakomera Yehova Kutundudza Kristu? (Yes. 53:10), 8/15

Kodi Odandaulawo Mafuta Anadzozedwa Yesu Anali Ndani? 4/15

Magazi Ako Omwe, 10/15

Mkwiyo wa Ndani? (12:19), 3/15

Zotengedwa M’magazi? 6/15

MBONI ZA YEHOVA

Altiplano ku Peru, 11/15

Anafupidwa Atafufuza kwa Nthaŵi Yaitali (Denmark), 9/1

Buku la Danieli Lifotokozedwa! (Buku la Ulosi wa Danieli), 1/15

Chilumba cha Robinson Crusoe, 6/15

“Chitsanzo cha Mgwirizano,” 10/15

India, 5/15

Italy, 1/15

Kudera Lamapiri la Chiapas (Mexico), 12/15

Kulengeza Ufumu ku Fiji, 9/15

Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15

Kusodza Anthu ku Nyanja ya Aegean, 4/15

Mamembala Atsopano a Bungwe Lolamulira, 1/1

Matupi Aang’ono, Mitima Yabwino, 2/15

Misonkhano Yachigawo yakuti “Mawu Aulosi a Mulungu,” 1/15

Mtima Wamataya Umadzetsa Chimwemwe (zopereka), 11/1

Poponderezedwa ndi Anazi (Netherlands), 4/1

Senegal, 3/15

Taiwan, 7/15

Tuvalu, 12/15

Ulendo wa ku Zilumba za M’nyanja ya Pacific—Kuntchito! 8/15

MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU

Abusa Achikristu, ‘Tsegulani Mtima Wanu’! 7/1

Kodi Anthu Achiwawa Mumawaona Monga Momwe Mulungu Amawaonera? 4/15

Kodi Kukhala Mkristu N’chiyani? 6/1

Kodi Kupambana Mumati N’kutani? 11/1

Kodi Mukupindula ndi Zitsanzo Zabwino? 7/1

Kodi Mumadziona Motani? 1/15

Kodi Mumatani Pakakhala Kusamvana? 8/15

Kodi N’chifukwa Chiyani Alibe Ana? 8/1

Kodi Ndinu Mkristu ‘Wokhwima Ndithu’? 8/15

Kodi Ndinu Wozindikira? 10/1

Kudzichepetsa—Mkhalidwe Umene Umalimbikitsa Mtendere, 3/15

Kufunafuna Yehova ndi Mtima Wokonzekera, 3/1

Kukhala Oganiza Bwino pa Zoyembekeza Zathu, 8/1

Kulemekeza Ulamuliro, 8/1

Kupanga Mzimu Woyera Kukhala Mthandizi Wanga, 10/15

Maukwati Osangalatsa Amene Amalemekeza Yehova, 5/1

Mmene Mungayandikirire kwa Mulungu, 10/15

Mukhoza Kudzisunga M’dziko Lachiwerewereli (Miy. 5), 7/15

Mukudzivomereza Nokha kwa Ena, 4/15

N’chifukwa Chiyani Mumatumikira Mulungu? 12/15

N’kukhaliranji Wodzimana? 9/15

Nyimbo Zomwe Zimakondweretsa Mulungu, 6/1

Pangani Ubwenzi Wathithithi ndi Yehova (Miy. 3), 1/15

Pezani Chitonthozo M’nyonga ya Yehova, 4/15

“Sunga Malangizo Anga, Nukhale ndi Moyo” (Miy. 7), 11/15

“Tchinjiriza Mtima Wako” (Miy. 4), 5/15

Tetezani Dzina Lanu, (Miy. 6), 9/15

Timafunikira Gulu Lolinganizidwa la Yehova, 1/1

Tumikirani Mulungu ndi Mzimu Wofunitsitsa, 11/15

Uphungu Wanzeru wa Mayi (Miy. 31), 2/1

MBIRI YA MOYO WANGA

Anandidalitsa ndi Choloŵa Chapadera (C. Allen), 10/1

Kukumbukira Mlengi Wathu Kuyambira Paunyamata (D. Hibshman), 1/1

Kusafuna Zambiri M’moyo Potumikira Yehova (C. Moyer), 3/1

Kusiya Ntchito Yopanga Zida Kuyamba Ntchito Yopulumutsa Miyoyo (I. Ismailidis), 8/1

Kuthokoza Yehova—Kupyolera mu Utumiki wa Nthaŵi Zonse! (S. Reynolds), 5/1

Ndinathandizidwa Kuthetsa Manyazi (R. Ulrich), 6/1

“N’takhala ndi Chikhulupiriro Chosafooka”! (H. Müller), 11/1

Nthaŵi Zonse Yehova Amafupa Anthu Ake Okhulupirika V. Duncombe), 9/1

“Simudziŵa Chimene Chidzagwa Maŵa” (H. Jennings), 12/1

Wonyamula Kuunika ku Mayiko Ambiri (G. Young), 7/1

Yehova Ndiye Pothaŵirapo Panga ndi Mphamvu Yanga (M. Filteau), 2/1

NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA

Akristu Amapeza Chimwemwe Potumikira, 11/15

Chirikizani Chiphunzitso Chaumulungu Molimbika, 5/1

Chiyembekezo cha Chiukiriro N’champhamvu, 7/15

Chiyembekezo cha Chiukiriro N’chotsimikizirika! 7/15

Choloŵa Chathu Chamtengo Wapatali—Kodi Chimatanthauzanji kwa Inu? 9/1

“Dikirani,” 1/15

Dziko Latsopano—Kodi Mudzakhalamo? 4/15

‘Dzipulumutseni Nokha Ndi Iwo Akumva Inu,’ 6/1

“Funani Yehova, ndi Mphamvu Yake,” 3/1

Imani Amphumphu ndi Otsimikiza Kotheratu, 12/15

Imvani Chimene Mzimu Unena, 5/1

“Inu Nonse Muli Abale,” 6/15

Khalanibe ndi “Chiyembekezo cha Chipulumutso” Choŵala! 6/1

Khalani ndi Chikhulupiriro M’mawu Aulosi a Mulungu! 5/15

Kodi Atumiki a Mulungu Ndani Lerolino? 11/15

Kodi Muli ndi “Mtima Wa Kristu”? 2/15

Kodi Mwasonkhezeredwa Kukhala Monga Yesu? 2/15

Kodi Oipa Adzakhalabe Kwa Utali Wotani? 2/1

Kodi Zikumbutso za Yehova Mumazikonda Kwambiri? 12/1

Kudzikuza Kumadzetsa Manyazi, 8/1

Kudziŵa “Mtima wa Kristu,” 2/15

Kufesa Mbewu za Choonadi cha Ufumu, 7/1

Kupanga Zinthu Zonse Kukhala Zatsopano—Monga Kunanenedwera, 4/15

Kupatula Nthaŵi Yoŵerenga ndi Kuphunzira, 10/1

Kuphunzira—N’kothandiza ndi Kokondweretsa, 10/1

Kusangalala Mwa Mulungu wa Chipulumutso Chathu, 2/1

Kutumikira Limodzi ndi Mlonda, 1/1

Kuŵerenga Baibulo—N’kopindulitsa ndi Kosangalatsa, 10/1

Labadirani Mawu Aulosi a Mulungu, 4/1

Labadirani Mawu Aulosi a Mulungu a M’tsiku Lathu, 5/15

Lalikani Uthenga Wabwino Mwachangu, 7/1

Lemekezani Anthu Opatsidwa Ulamuliro Pa Inu, 6/15

Lingaliro Laumulungu la Khalidwe Loyera, 11/1

Mmene Yehova Akutitsogolera, 3/15

‘Mulungu, Tumizani Kuunika Kwanu,’ 3/15

Mungakhalebe ndi Khalidwe Loyera, 11/1

Nsembe Zimene Zinakondweretsa Mulungu, 8/15

Nsembe Zotamanda Zimene Zimakondweretsa Yehova, 8/15

“Nthaŵi Yake Siinafike,” 9/15

“Nzeru Ili ndi Odzichepetsa,” 8/1

Omenyana Ndi Mulungu Sadzapambana, 4/1

Sonyezani Mtima wa Kristu, 9/1

Sonyezani Mtima Wodikira! 9/1

Thandizani Ena Kuyenda Moyenera Yehova, 12/15

Ufumu wa Mulungu—Ulamuliro Watsopano wa Dziko Lapansi, 10/15

“Wamng’ono” Wasanduka “Chikwi,” 1/1

“Yafika Nthaŵi”! 9/15

Yehova Amapereka Mphamvu kwa Wotopa, 12/1

Yehova—Iye Amene Ali Wolimba Mphamvu, 3/1

Yehova Sadzachedwa, 2/1

Zimene Ufumu wa Mulungu Udzachita, 10/15

“Zinthu Zofunika” Zikudzaza Nyumba ya Yehova, 1/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

“Abale a ku Poland,” 1/1

Antiokeya (Syria), 7/15

Chidani, Kodi chidzatha? 8/15

Chikhulupiriro Chingasinthe Moyo Wanu, 1/1

Chinsinsi cha Chipambano, 2/1

Cyril Lucaris—Mwamuna Yemwe Anaona Baibulo Kukhala Lofunika, 2/15

Dziko Lopanda Nkhaŵa, 9/15

Kodi Apezanji pa Yezreeli? 3/1

Kodi Malangizo Abwino Mungawapeze Kuti? 6/1

Kodi Muyenera Kufufuza za Zipembedzo Zina? 10/15

Kodi Muyenera Kuwakhulupirira? 12/1

Kodi Mzimu wa Mulungu Umagwira Ntchito Motani Lerolino? 4/1

Kugwira Ntchito “M’munda”—Nyengo Yotuta Isanafike, 10/15

Kukongola kwa M’kati, 11/15

Kupemphera Kumathandizadi? 11/15

Kuthetsa Ziphuphu, 5/1

‘Kuzungulira Guwa la Nsembe Lanu,’ 5/1

Makhalidwe a M’Baibulo Ndiwo Ali Abwino Koposa, 11/1

Malo Ongoyeserapo Anthu, 10/1

‘Mbuzi ya Kumapiri ya Maonekedwe Osiririka,’ 10/1

Mgwirizano pa Kupembedza Ukuoneka kuti Ungatheke? 12/1

Miyambo ya Khirisimasi—Kodi Ndi Yachikristu? 12/15

Mmene Mungapezere Mabwenzi, 12/1

Mmene Moyo Wanu Ungakhalire ndi Tanthauzo Lalikulu, 7/15

Moyo Wangwiro Si Loto Chabe! 6/15

Mtendere wa Dziko Lonse Udzakhalapo Motani? 11/1

Mtengo wa Azitona, 5/15

Mulungu Amayankha Mapemphero, 3/1

Mumadziŵa Kudikira? 9/1

Mumakhulupirira Zomwe Simungathe Kuziona? 6/15

Mungapeze Mtendere wa Mumtima, 7/1

Mverani Chenjezo! 2/15

Mwamuna Wachitsanzo Chabwino Amene Anavomera Kum’langiza, (Yobu) 3/15

N’kugonjetseranji Malingaliro Osafuna Kulakwitsa Kanthu? 6/15

“Nthaŵi za Kukonzanso” Zayandikira! 9/1

Osuliza, 7/15

Nyama za M’Baibulo, 2/15

Tingaphunzire ku Banja Loyamba la Anthu, 11/15

Ufiti?, 4/1

Wozunza Aona Kuunika Kwakukulu (Paulo), 1/15

Yosiya, 9/15

OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA

2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 8/1, 9/1, 12/1

YEHOVA

Kodi Yehova Adzakukumbukirani Motani? 2/1

Mulungu Amayankha Mapemphero, 3/1

Wamkulu Kuposa Mitima Yathu, 5/1

YESU KRISTU

Mmene Yesu Kristu Angatithandizire, 3/15

    Mabuku gha Chitumbuka (1982-2023)
    Fumani
    Njirani
    • Chitumbuka
    • Tumizgani
    • Ivyo Mukukhumba
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Malango
    • Phangano
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Njirani
    Tumizgani