Mateyu 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 n’kunena kuti, ‘Pa chifukwa chimenechi mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi’?+
5 n’kunena kuti, ‘Pa chifukwa chimenechi mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi’?+