AUGUST 4-10
MIYAMBO 25
Nyimbo Na. 154 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
Yesu ali mu sunagoge ku Nazareti ndipo akulankhula mawu okoma omwe agometsa anthu
1. Mfundo Zothandiza Kuti Tizilankhula Bwino
(10 min.)
Muzisankha nthawi yabwino kuti mulankhule (Miy 25:11; w15 12/15 19 ¶6-7)
Muzilankhula mokoma mtima (Miy 25:15; w15 12/15 21 ¶15-16; onani chithunzi)
Muzilankhula mawu olimbikitsa (Miy 25:25; w95 4/1 17 ¶8)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Miy 25:1-17 (th phunziro 10)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Yambani kukambirana ndi munthu amene akuoneka kuti wakhumudwa. (lmd phunziro 3 mfundo 3)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthuyo wakuuzani kuti ali ndi chipembedzo chake ndipo sangasinthe. (lmd phunziro 8 mfundo 4)
6. Nkhani
(5 min.) ijwyp nkhani na. 23—Mutu: Kodi Ndingatani Ngati Anthu Ena Akukonda Kunena za Ine? (th phunziro 13)
Nyimbo Na. 123
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 6, mawu ofotokoza chigawo 3 komanso mutu 7