Genesis 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo dzina lake udzamutche Isaki.+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, limene lidzakhala mpaka kalekale kwa mbewu yake yobwera pambuyo pa iye.+ Genesis 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Patapita nthawi, Isaki anakhala wolemera, ndipo chuma chake chinapitiriza kuchuluka mpaka anakhala wolemera kwambiri.+
19 Pamenepo Mulungu anati: “Ndithu Sara mkazi wako adzakuberekera mwana wamwamuna ndipo dzina lake udzamutche Isaki.+ Ndidzakhazikitsa pangano ndi iye, limene lidzakhala mpaka kalekale kwa mbewu yake yobwera pambuyo pa iye.+
13 Patapita nthawi, Isaki anakhala wolemera, ndipo chuma chake chinapitiriza kuchuluka mpaka anakhala wolemera kwambiri.+