Genesis 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Patapita nthawi, Abimeleki anafika kwa iye kuchokera ku Gerari. Anafika limodzi ndi Ahuzati bwenzi lake lapamtima, komanso Fikolo mkulu wa asilikali ake.+
26 Patapita nthawi, Abimeleki anafika kwa iye kuchokera ku Gerari. Anafika limodzi ndi Ahuzati bwenzi lake lapamtima, komanso Fikolo mkulu wa asilikali ake.+