Oweruza 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yefita anauza akulu+ a ku Giliyadiwo kuti: “Kodi si inu amene munadana nane ndi kundithamangitsa m’nyumba ya bambo anga?+ N’chifukwa chiyani tsopano mwabwera kwa ine pamene mwakumana ndi mavuto?”+
7 Koma Yefita anauza akulu+ a ku Giliyadiwo kuti: “Kodi si inu amene munadana nane ndi kundithamangitsa m’nyumba ya bambo anga?+ N’chifukwa chiyani tsopano mwabwera kwa ine pamene mwakumana ndi mavuto?”+