Genesis 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero Isaki anatumiza Yakobo, ndipo iye ananyamuka ulendo wopita ku Padana-ramu. Anapita kwa Labani mwana wa Betuele, Msiriya.+ Labaniyo anali mlongo wake wa Rabeka,+ mayi ake a Yakobo ndi Esau.+
5 Chotero Isaki anatumiza Yakobo, ndipo iye ananyamuka ulendo wopita ku Padana-ramu. Anapita kwa Labani mwana wa Betuele, Msiriya.+ Labaniyo anali mlongo wake wa Rabeka,+ mayi ake a Yakobo ndi Esau.+